2 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Itana mayi wachisunemu+ uja.” Choncho iye anamuitana kuti adzaime pamaso pa Elisa. 2 Mafumu 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawiyo, mfumu inali ikulankhula ndi Gehazi+ mtumiki wa munthu wa Mulungu woona, kuti: “Ndifotokozere zinthu zonse zazikulu zimene Elisa wachita.”+
12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Itana mayi wachisunemu+ uja.” Choncho iye anamuitana kuti adzaime pamaso pa Elisa.
4 Pa nthawiyo, mfumu inali ikulankhula ndi Gehazi+ mtumiki wa munthu wa Mulungu woona, kuti: “Ndifotokozere zinthu zonse zazikulu zimene Elisa wachita.”+