20 Kenako Gehazi,+ amene anali kutumikira Elisa, munthu wa Mulungu woona+ uja, ananena mumtima mwake kuti: “Mbuyanga wangomusiya Namani+ Msiriya uja osalandira zimene anabweretsa. Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ ndim’thamangira kuti ndikatengeko zinthu zina kwa iye.”+