2 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Itana mayi wachisunemu+ uja.” Choncho iye anamuitana kuti adzaime pamaso pa Elisa.
12 Ndiyeno Elisa anauza mtumiki wake Gehazi+ kuti: “Itana mayi wachisunemu+ uja.” Choncho iye anamuitana kuti adzaime pamaso pa Elisa.