Machitidwe 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Moti anthu anali kutenga ngakhale mipango yopukutira thukuta ndi maepuloni amene akhudza thupi la Paulo n’kupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo anali kutheratu. Mizimu yoipa nayonso inali kutuluka.+
12 Moti anthu anali kutenga ngakhale mipango yopukutira thukuta ndi maepuloni amene akhudza thupi la Paulo n’kupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo anali kutheratu. Mizimu yoipa nayonso inali kutuluka.+