Machitidwe 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Moti anthu ankatenga ngakhale tinsalu ndi zovala* zimene zakhudza thupi la Paulo nʼkupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo ankatheratu. Nayonso mizimu yoipa inkatuluka.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 162 Nsanja ya Olonda,11/15/1991, tsa. 5
12 Moti anthu ankatenga ngakhale tinsalu ndi zovala* zimene zakhudza thupi la Paulo nʼkupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo ankatheratu. Nayonso mizimu yoipa inkatuluka.+