Machitidwe 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Moti anthu anali kutenga ngakhale mipango yopukutira thukuta ndi maepuloni amene akhudza thupi la Paulo n’kupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo anali kutheratu. Mizimu yoipa nayonso inali kutuluka.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:12 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 162 Nsanja ya Olonda,11/15/1991, tsa. 5
12 Moti anthu anali kutenga ngakhale mipango yopukutira thukuta ndi maepuloni amene akhudza thupi la Paulo n’kupita nazo kwa odwala,+ ndipo matenda awo anali kutheratu. Mizimu yoipa nayonso inali kutuluka.+