Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ana akewa sanatsatire chitsanzo chake,+ koma anali okonda kupeza phindu mwachinyengo,+ ndipo anali kulandira ziphuphu+ ndi kupotoza chiweruzo.+

  • Yesaya 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Akalonga ako ndi aliuma ndipo ndi anzawo a mbala.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu+ ndipo amafunafuna mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+

  • Yesaya 5:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsoka kwa anthu amene amanena kuti woipa ndi wolungama chifukwa cholandira chiphuphu,+ ndiponso kwa amene amanena kuti wolungama ndi wolakwa.+

  • Ezekieli 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena