Miyambo 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mphatso yoperekedwa mobisa imathetsa mkwiyo,+ ndipo chiphuphu chopereka mobisa chimathetsa+ ukali waukulu. Mlaliki 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuponderezedwa kumapangitsa munthu wanzeru kuchita zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mphatso+ ikhoza kuwononga mtima wa munthu.+
14 Mphatso yoperekedwa mobisa imathetsa mkwiyo,+ ndipo chiphuphu chopereka mobisa chimathetsa+ ukali waukulu.
7 Kuponderezedwa kumapangitsa munthu wanzeru kuchita zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mphatso+ ikhoza kuwononga mtima wa munthu.+