Deuteronomo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usamapotoze chiweruzo.+ Usamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ ndi kupotoza mawu a anthu olungama. Miyambo 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wopeza phindu mwachinyengo amabweretsa tsoka panyumba pake,+ koma wodana ndi ziphuphu ndi amene adzakhalebe ndi moyo.+
19 Usamapotoze chiweruzo.+ Usamakondere+ kapena kulandira chiphuphu, chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu maso a anthu anzeru+ ndi kupotoza mawu a anthu olungama.
27 Munthu wopeza phindu mwachinyengo amabweretsa tsoka panyumba pake,+ koma wodana ndi ziphuphu ndi amene adzakhalebe ndi moyo.+