Ekisodo 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+ 1 Samueli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana akewa sanatsatire chitsanzo chake,+ koma anali okonda kupeza phindu mwachinyengo,+ ndipo anali kulandira ziphuphu+ ndi kupotoza chiweruzo.+ Miyambo 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Woipa amatenga chiphuphu mobisa,+ kuti akhotetse njira za chiweruzo.+
8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+
3 Ana akewa sanatsatire chitsanzo chake,+ koma anali okonda kupeza phindu mwachinyengo,+ ndipo anali kulandira ziphuphu+ ndi kupotoza chiweruzo.+