Yesaya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+ Mika 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya Yakobo komanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+ amene mukuipidwa ndi chilungamo ndiponso amene mukupotoza chilichonse chowongoka.+
14 Yehova adzaweruza achikulire pakati pa anthu ake ndi akalonga ake.+ “Inuyo mwatentha munda wa mpesa. Zinthu zimene zinabedwa kwa anthu ovutika zili m’nyumba zanu.+
9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya Yakobo komanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+ amene mukuipidwa ndi chilungamo ndiponso amene mukupotoza chilichonse chowongoka.+