Levitiko 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+ Deuteronomo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Yeremiya 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo anenepa+ ndipo matupi awo asalala. Achitanso zinthu zoipa zosawerengeka. Iwo sanaweruze mlandu wa munthu aliyense mwachilungamo,+ ngakhale mlandu wa mwana wamasiye,*+ pofuna kuti zinthu ziwayendere bwino.+ Iwo sanachitire chilungamo munthu wosauka.’”
15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ n’kunyansidwa ndi zigamulo zanga, moti mwakana kutsatira malamulo anga onse, n’kufika pophwanya pangano langa,+
19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
28 Iwo anenepa+ ndipo matupi awo asalala. Achitanso zinthu zoipa zosawerengeka. Iwo sanaweruze mlandu wa munthu aliyense mwachilungamo,+ ngakhale mlandu wa mwana wamasiye,*+ pofuna kuti zinthu ziwayendere bwino.+ Iwo sanachitire chilungamo munthu wosauka.’”