Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+

      Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendere

      Wofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+

  • Salimo 73:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+

      Iwo achulukitsa chuma chawo.+

  • Yeremiya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu Yehova, ndinu Mulungu wolungama.+ Ndikabweretsa dandaulo kwa inu, ndipo ndikalankhula za chiweruzo chanu, mumachita chilungamo. Koma n’chifukwa chiyani anthu oipa, zinthu zikuwayendera bwino?+ N’chifukwa chiyani onse ochita chinyengo amakhala opanda nkhawa iliyonse?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena