Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mahema a anthu olanda amakhala opanda nkhawa,+

      Ndipo anthu okwiyitsa Mulungu amakhala pa mtendere

      Wofanana ndi wa munthu amene watenga mulungu* m’manja mwake.+

  • Yobu 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 N’chifukwa chiyani oipa amakhalabe ndi moyo,+

      Amakalamba komanso amalemera kwambiri?+

  • Salimo 37:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Usapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa.+

      Usakhumbe kukhala ngati anthu ochita zosalungama.+

  • Salimo 73:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pakuti ndinachitira nsanje anthu odzitukumula,+

      Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+

  • Yeremiya 5:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iwo anenepa+ ndipo matupi awo asalala. Achitanso zinthu zoipa zosawerengeka. Iwo sanaweruze mlandu wa munthu aliyense mwachilungamo,+ ngakhale mlandu wa mwana wamasiye,*+ pofuna kuti zinthu ziwayendere bwino.+ Iwo sanachitire chilungamo munthu wosauka.’”

  • Malaki 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Panopa anthu odzikuza tikuwatcha odala.+ Komanso anthu ochita zoipa zinthu zikuwayendera bwino.+ Iwo ayesa Mulungu koma sakulandira chilango.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena