Salimo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+ Salimo 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti pamene anali moyo anali kutamanda moyo wake,+(Ndipo anthu adzakutamanda chifukwa chakuti walemera)+
3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+
18 Pakuti pamene anali moyo anali kutamanda moyo wake,+(Ndipo anthu adzakutamanda chifukwa chakuti walemera)+