Miyambo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+ Miyambo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usamasirire anthu oipa,+ ndipo usamasonyeze kuti ukusirira kukhala pagulu lawo,+ Miyambo 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Usamapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa. Usamasirire anthu oipa,+