Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+ Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+ Salimo 145:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova ndi wolungama m’njira zake zonse,+Ndipo ndi wokhulupirika m’ntchito zake zonse.+ Zefaniya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+
25 Simungachite zimenezo, kupha munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama aone zofanana ndi woipa.+ Simungachite zimenezo ayi.+ Kodi Woweruza wa dziko lonse lapansi sadzachita cholungama?”+
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+