Zefaniya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndi wolungama mumzindawo+ ndipo salakwitsa. Mʼmawa uliwonse iye amadziwitsa anthu chilungamo chake,+Moti mofanana ndi kuwala, chilungamocho sichisowa. Koma wosalungama sachita manyazi.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 22
5 Yehova ndi wolungama mumzindawo+ ndipo salakwitsa. Mʼmawa uliwonse iye amadziwitsa anthu chilungamo chake,+Moti mofanana ndi kuwala, chilungamocho sichisowa. Koma wosalungama sachita manyazi.+