Zefaniya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 22
5 Yehova anali wolungama mkati mwa mzindawo+ ndipo sanali kuchita zosalungama.+ M’mawa uliwonse iye anali kuchita chilungamo chake+ moti sichinali kusowa mpaka m’bandakucha,+ koma wosalungamayo sanali kuchita manyazi.+