Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+ Aroma 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ndipo akuonetsa chilungamo chake+ m’nyengo inoyo pakutcha munthu amene ali ndi chikhulupiriro mwa Yesu kuti ndi wolungama.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
4 Iye amakonda chilungamo ngati mmene mfumu yamphamvu imachitira.+Inu mwakhazikitsa kulungama.+Mwakhazikitsa chiweruzo ndi chilungamo pakati pa ana a Yakobo.+
26 ndipo akuonetsa chilungamo chake+ m’nyengo inoyo pakutcha munthu amene ali ndi chikhulupiriro mwa Yesu kuti ndi wolungama.+