Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+ Aroma 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero, mmene zinakhalira kuti mwa uchimo umodzi anthu kaya akhale amtundu wotani anaweruzidwa kukhala ochimwa,+ momwemonso mwa kuchita chinthu chimodzi cholungamitsa,+ anthu kaya akhale amtundu wotani+ akuyesedwa olungama kuti akhale ndi moyo.+
14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+
18 Chotero, mmene zinakhalira kuti mwa uchimo umodzi anthu kaya akhale amtundu wotani anaweruzidwa kukhala ochimwa,+ momwemonso mwa kuchita chinthu chimodzi cholungamitsa,+ anthu kaya akhale amtundu wotani+ akuyesedwa olungama kuti akhale ndi moyo.+