Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+ Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+ 1 Timoteyo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene chifuniro chake n’chakuti anthu, kaya akhale a mtundu wotani,+ apulumuke+ ndi kukhala odziwa choonadi+ molondola.+
16 Pakuti sindichita nawo manyazi+ uthenga wabwino. Kunena zoona, uthengawo ndi mphamvu+ ya chipulumutso imene Mulungu amaipereka kwa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba kwa Myuda+ kenako kwa Mgiriki.+
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi.+ Nonsenu ndinu munthu mmodzi mwa Khristu Yesu.+
4 amene chifuniro chake n’chakuti anthu, kaya akhale a mtundu wotani,+ apulumuke+ ndi kukhala odziwa choonadi+ molondola.+