Miyambo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wosauka amene amachita zinthu mokhulupirika,Ali bwino kuposa munthu wolemera amene amachita zachinyengo.+
6 Munthu wosauka amene amachita zinthu mokhulupirika,Ali bwino kuposa munthu wolemera amene amachita zachinyengo.+