Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho Sauli anafa chifukwa cha kusakhulupirika kwake popeza anachita zosakhulupirika+ kwa Yehova. Iye sanasunge mawu a Yehova komanso anapita kukafunsa kwa wolankhula ndi mizimu.+

  • Salimo 40:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+

      Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,

      Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+

  • Salimo 101:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Sindidzaika maso anga pa chinthu chilichonse chopanda pake.+

      Ndimadana ndi zochita za opatuka pa choonadi.+

      Sindilola kuti zochita zawozo zindikhudze.+

  • Miyambo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 amene njira zawo ndi zokhota ndiponso amene ali achinyengo m’zochita zawo zonse.+

  • Yesaya 59:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwo amangonyalanyaza njira yamtendere,+ ndipo m’njira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.+ Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena