Miyambo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Njira zake n’zobweretsa chisangalalo ndipo misewu yake yonse ndi yamtendere.+ Luka 1:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”
79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”