Yesaya 59:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choonadi chikusowa+ ndipo aliyense wokana zoipa akusakazidwa.+ Yehova anaona zimenezi ndipo zinamuipira m’maso mwake poona kuti panalibe chilungamo.+ Amosi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa. Habakuku 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+
15 Choonadi chikusowa+ ndipo aliyense wokana zoipa akusakazidwa.+ Yehova anaona zimenezi ndipo zinamuipira m’maso mwake poona kuti panalibe chilungamo.+
12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.
4 “Choncho lamulo latha mphamvu ndipo anthu sakuchitanso chilungamo.+ Chilungamo chapotozedwa chifukwa anthu oipa akupondereza anthu olungama.+