Salimo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa cha anthu oipa amene akundipondereza.Adani a moyo wanga atsala pang’ono kundipeza.+ Amosi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’
4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’