Salimo 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+ Ezekieli 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+ Hoseya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Isiraeli wakhala wamakani* ngati ng’ombe yamakani.+ Choncho kodi Yehova angawawete ngati nkhosa yamphongo yaing’ono pamalo otakasuka?
12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+
18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+
16 Isiraeli wakhala wamakani* ngati ng’ombe yamakani.+ Choncho kodi Yehova angawawete ngati nkhosa yamphongo yaing’ono pamalo otakasuka?