Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anamudyetsanso mafuta a mkaka wa ng’ombe ndi mkaka wa nkhosa,+

      Pamodzi ndi mafuta a nkhosa.

      Anamudyetsa nkhosa zamphongo za ku Basana, mbuzi zamphongo,+

      Pamodzi ndi tirigu wabwino koposa ngati mafuta okuta impso.+

      Ndipo anali kumwa magazi a mphesa monga vinyo.+

  • Salimo 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+

      Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+

  • Amosi 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena