Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+

  • Ezekieli 39:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+

  • Amosi 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’

  • Mateyu 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena