Genesis 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamanga bulu wake wamphongo pamtengo wa mpesa, ndi kamwana ka bulu wake wamkazi pamtengo wa mpesa wabwino, ndithu, adzachapa zovala zake m’vinyo, ndi malaya ake m’madzi ofiira a mphesa.+
11 Atamanga bulu wake wamphongo pamtengo wa mpesa, ndi kamwana ka bulu wake wamkazi pamtengo wa mpesa wabwino, ndithu, adzachapa zovala zake m’vinyo, ndi malaya ake m’madzi ofiira a mphesa.+