Yesaya 63:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 N’chifukwa chiyani zovala zanu zili zofiira, ndipo n’chifukwa chiyani zovala zimene mwavala zikuoneka ngati za munthu woponda mphesa m’choponderamo mphesa?+
2 N’chifukwa chiyani zovala zanu zili zofiira, ndipo n’chifukwa chiyani zovala zimene mwavala zikuoneka ngati za munthu woponda mphesa m’choponderamo mphesa?+