Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoweli 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Yambani kumweta ndi chikwakwa,+ pakuti zokolola zacha.+ Bwerani, tsikirani kuno, pakuti moponderamo mphesa mwadzaza.+ Malo ogweramo vinyo wake asefukira, pakuti zoipa za anthu a mitundu ina zachuluka kwambiri.+

  • Chivumbulutso 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+

  • Chivumbulutso 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena