Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako amuna awiri opanda pake anabwera n’kukhala patsogolo pa Naboti. Ndiyeno amuna opanda pakewo anayamba kupereka umboni wotsutsana ndi Naboti pamaso pa anthuwo, wakuti: “Naboti watemberera Mulungu ndi mfumu!”+ Pambuyo pake anamutulutsira kunja kwa mzindawo n’kumuponya miyala mpaka anafa.+

  • Salimo 94:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kodi inu mudzagwirizana ndi olamulira ankhanza,+

      Pamene akuyambitsa mavuto mwa kupanga malamulo?+

  • Yesaya 59:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ife taphwanya malamulo ndipo tamukana Yehova.+ Tabwerera m’mbuyo n’kumusiya Mulungu wathu. Tanena zinthu zopondereza ena ndi zopanduka.+ Taganiza mawu achinyengo mumtima mwathu n’kumawalankhula chapansipansi.+

  • Hoseya 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Iwo amalankhula mawu opanda pake, amachita malumbiro abodza,+ amachita mapangano+ ndipo kusalungama kwafalikira ngati zomera zakupha m’mizere ya m’munda.+

  • Amosi 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mukuweruza mopanda chilungamo,+ choncho moyo wakhala wowawa ndi wosautsa kwa anthu, pakuti inuyo mwakana chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena