Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Cholinga cha pangano limeneli n’chakuti, pakati panu pasapezeke mwamuna, mkazi, banja kapena fuko limene mtima wake ukupatuka kusiyana ndi Yehova Mulungu wathu, ndi kupita kukatumikira milungu ya mitundu inayo,+ kuti pakati panu pasapezeke muzu wotulutsa chomera chakupha ndi chitsamba chowawa.+

  • Yesaya 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ine ndine Yehova wa makamu ndipo Isiraeli ndi munda wanga wa mpesa.+ Amuna a ku Yuda ndiwo mitengo ya mpesa imene ndinali kuikonda.+ Ine ndinali kuyembekezera chilungamo+ koma ndinaona anthu akuphwanya malamulo. Ndinali kuyembekezera zolungama koma ndinaona anthu akulira.”+

  • Amosi 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mukuweruza mopanda chilungamo,+ choncho moyo wakhala wowawa ndi wosautsa kwa anthu, pakuti inuyo mwakana chilungamo.+

  • Amosi 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Kodi mahatchi angathamange pathanthwe, kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ng’ombe? Anthu inu mwakana chilungamo,+ choncho mwachititsa moyo wa anthu kukhala wowawa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena