Deuteronomo 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+ Deuteronomo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 moti akupita kukalambira milungu ina ndi kuigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ chinthu chimene ine sindinakulamuleni,+ Aheberi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+
16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+
3 moti akupita kukalambira milungu ina ndi kuigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ chinthu chimene ine sindinakulamuleni,+
12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+