Deuteronomo 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+ Deuteronomo 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma mtima wako ukatembenukira kwina ndipo sukumvera,+ moti wanyengeka, n’kugwadira milungu ina ndi kuitumikira,+
19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+
17 “Koma mtima wako ukatembenukira kwina ndipo sukumvera,+ moti wanyengeka, n’kugwadira milungu ina ndi kuitumikira,+