Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Musamale kuti musakweze maso anu kuthambo ndi kuona dzuwa, mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la zinthu zakuthambo, zimene Yehova Mulungu wanu wazipereka kwa anthu onse okhala pansi pa thambo lonse,+ n’kunyengeka nazo, kuzigwadira ndi kuyamba kuzitumikira.+

  • Deuteronomo 31:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pakuti ndikudziwa bwino kuti pambuyo pa imfa yanga, mosakayikira mudzachita zinthu zokuwonongetsani+ ndipo mudzapatuka ndi kusiya njira imene ndakulamulani kuyendamo. Pamapeto pake tsoka+ lidzakugwerani, chifukwa mudzachita zoipa pamaso pa Yehova ndi kumulakwira ndi ntchito za manja anu.”+

  • Salimo 96:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa milungu yonse ya anthu a mitundu ina ndi milungu yopanda pake,+

      Koma Yehova ndiye anapanga kumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena