Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+

      Si ana ake, chilemacho n’chawo.+

      Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+

  • Oweruza 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno zinali kuchitika kuti woweruza akamwalira, ana a Isiraeli anali kupatuka ndi kuchita zinthu zowawonongetsa kuposanso makolo awo. Anali kuchita zimenezi mwa kutsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso khalidwe lawo la unkhutukumve.+

  • Hoseya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Aisiraeli azama nazo zinthu zowononga+ ngati m’masiku a Gibeya.+ Mulungu adzakumbukira zolakwa zawo+ ndipo adzawalanga chifukwa cha machimo awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena