Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+ Yesaya 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Podziwa kuti ndinu olimba,+ ndi kuti mtsempha wa khosi lanu uli ngati chitsulo,+ ndiponso kuti mphumi yanu ili ngati mkuwa,+
8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+
4 Podziwa kuti ndinu olimba,+ ndi kuti mtsempha wa khosi lanu uli ngati chitsulo,+ ndiponso kuti mphumi yanu ili ngati mkuwa,+