Ekisodo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova anauzanso Mose kuti: “Ndawayang’ana anthu amenewa, ndipo ndaona kuti ndi anthu ouma khosi.+ Deuteronomo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mitima yanu muichite mdulidwe+ ndipo musakhalenso ouma khosi.+ 2 Mafumu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.
14 Koma iwo sanamvere. M’malomwake anaumitsa makosi awo,+ ngati mmene makolo awo anaumitsira makosi awo. Makolo awowo sanasonyeze chikhulupiriro+ mwa Yehova Mulungu wawo.