Yeremiya 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+ Yeremiya 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo amangiranso Baala malo okwezeka kuti azitentherapo ana awo aamuna monga nsembe zopsereza zathunthu zoperekedwa kwa Baala.+ Ine sindinawalamule zimenezi kapena kuzitchula,+ ndipo sindinaziganizirepo mumtima mwanga.”’+
18 Ana aamuna akutola nkhuni, abambo akuyatsa moto ndipo akazi akukanda ufa kuti apange makeke okapereka nsembe kwa ‘mfumukazi yakumwamba.’+ Ndipo akuthira pansi nsembe zachakumwa+ kwa milungu ina kuti andikhumudwitse.+
5 Iwo amangiranso Baala malo okwezeka kuti azitentherapo ana awo aamuna monga nsembe zopsereza zathunthu zoperekedwa kwa Baala.+ Ine sindinawalamule zimenezi kapena kuzitchula,+ ndipo sindinaziganizirepo mumtima mwanga.”’+