Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 57:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Gawo lako linali pamodzi ndi miyala yosalala ya m’chigwa.+ Iwo ndiwo anali gawo lako.+ Iwe unawathirira nsembe yachakumwa,+ ndiponso unawapatsa mphatso. Kodi ine ndingadzitonthoze ndi zinthu zimenezo?+

  • Yeremiya 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ‘Nyumba za mu Yerusalemu ndi nyumba za mafumu a Yuda zidzakhala zodetsedwa ngati Tofeti.+ Zimenezi ndi nyumba zonse zimene pamadenga ake anali kufukizirapo nsembe zautsi kwa makamu akumwamba+ ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa milungu ina.’”+

  • Ezekieli 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Komabe ine ndinawalowetsa m’dziko+ limene ndinawalumbirira nditakweza dzanja langa kuti ndidzawapatsa.+ Koma ataona phiri lililonse lalitali+ ndi mtengo uliwonse wanthambi zambiri, anayamba kupereka nsembe zawo pamenepo+ ndi zopereka zawo zochititsa mseru. Analinso kufukiza nsembe zafungo lokhazika mtima pansi+ ndi kuthira nsembe zawo zachakumwa pamalo amenewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena