Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako mfumuyo inagumula maguwa ansembe amene anali padenga la chipinda chapadenga+ cha Ahazi, amene mafumu a Yuda anamanga. Inagumulanso maguwa ansembe+ amene Manase anamanga pamabwalo awiri a nyumba ya Yehova. Itatero, inawaperapera komweko ndipo fumbi lake inakaliwaza kuchigwa* cha Kidironi.

  • 2 Mafumu 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inaphwanyaphwanya+ zipilala zopatulika ndipo inagwetsanso mizati yopatulika. Pamalo pamene panali zimenezi inadzazapo mafupa a anthu.

  • Salimo 79:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+

      Aipitsa kachisi wanu woyera.+

      Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+

  • Ezekieli 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndidzazipereka m’manja mwa alendo kuti zikhale zawo ndi kwa anthu oipa a padziko lapansi kuti azitenge,+ ndipo adzaziipitsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena