2 Mafumu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ m’mabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+ 2 Mbiri 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo+ m’mabwalo+ awiri a nyumba ya Yehova.+
5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ m’mabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+
5 Iye anamangira maguwa ansembe khamu lonse la zinthu zakuthambo+ m’mabwalo+ awiri a nyumba ya Yehova.+