Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 6:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.

  • 1 Mafumu 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kuzungulira bwalo lalikulu panali khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuchokera pansi, ndi mzere umodzi wa matabwa a mkungudza pamwamba pake. Bwalo lamkati+ la nyumba+ ya Yehova ndi khonde+ la nyumbayo, zinamangidwanso mofanana.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena