Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 27:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Ndiyeno upange bwalo+ la chihema chopatulika. Kumbali ya ku Negebu, chakum’mwera, bwalolo ulitchinge ndi mpanda wa nsalu za ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Mpandawo ukhale mikono 100 m’litali mwake kumbali imodziyo.

  • 1 Mafumu 6:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Kenako anamanga khoma la miyala yosema lotalika mizere itatu+ kuzungulira bwalo lamkati,+ ndipo anawonjezeranso mzere umodzi wa matabwa a mkungudza.

  • 2 Mbiri 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno anapanga bwalo+ la ansembe+ ndi bwalo lalikulu lamkati+ ndi zitseko za bwalo lalikululo. Zitsekozo anazikuta ndi mkuwa.

  • 2 Mbiri 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Solomo anapatula+ malo a pakati pa bwalo la nyumba ya Yehova, chifukwa pamenepo anaperekerapo nsembe zopsereza,+ ndi mafuta a nsembe zachiyanjano. Anatero popeza guwa lansembe lamkuwa+ limene iye anamanga linachepa, ndipo sipakanakwana nsembe yopsereza, nsembe yambewu,+ ndi mafuta oundana.+

  • Chivumbulutso 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena