Ezekieli 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anandipititsa kubwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyeramo+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka miyala. Pabwalo lowaka miyalalo panali zipinda zodyeramo zokwana 30.+
17 Kenako anandipititsa kubwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyeramo+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka miyala. Pabwalo lowaka miyalalo panali zipinda zodyeramo zokwana 30.+