Ezekieli 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kudzakhalenso malo okwana mikono 25,000 m’litali ndi mikono 10,000 m’lifupi.+ Malo amenewa adzakhale a Alevi, atumiki a pa Nyumbayo. Aleviwo adzakhale ndi zipinda 20 zodyeramo chakudya.+
5 “‘Kudzakhalenso malo okwana mikono 25,000 m’litali ndi mikono 10,000 m’lifupi.+ Malo amenewa adzakhale a Alevi, atumiki a pa Nyumbayo. Aleviwo adzakhale ndi zipinda 20 zodyeramo chakudya.+