Ezekieli 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anandipititsa mʼbwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyera*+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka. Pabwalo lowakalo panali zipinda zodyera zokwana 30. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 149/15/1988, ptsa. 26-27
17 Kenako anandipititsa mʼbwalo lakunja. Kumeneko ndinaona zipinda zodyera*+ ndipo pansi pa bwalo lonselo panali powaka. Pabwalo lowakalo panali zipinda zodyera zokwana 30.